Lamulo la Malo a Makolo 2016
Msonkhano Wodziwitsa Atsogoleri a ma Dipatimenti ndi Mabungwe a pa Boma
Mamembala a nthambi yoyendetsa chitukuko pa Boma ayenera kudziwa za lamulo la malo a makolo koyambirira kuti asankhe dera lomwe angakayambire ntchito zokhudza lamuloli.
Msonkhano Wodziwitsa Makomiti a ADC, VDC ndi Magulu a m’madera za Lamulo la Malo a Makolo